Ezekieli 12:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pakati pawo ndidzapulumutsapo amuna ochepa kuti asaphedwe ndi lupanga,+ njala, kapena miliri, n’cholinga chakuti akafotokoze za zinthu zawo zonse zonyansa+ pakati pa mitundu imene akakhaleko,+ ndipo adzadziwa kuti ine ndine Yehova.”
16 Pakati pawo ndidzapulumutsapo amuna ochepa kuti asaphedwe ndi lupanga,+ njala, kapena miliri, n’cholinga chakuti akafotokoze za zinthu zawo zonse zonyansa+ pakati pa mitundu imene akakhaleko,+ ndipo adzadziwa kuti ine ndine Yehova.”