Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 44:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Kenako Yehova sanathenso kupirira zimenezo chifukwa zochita zanu zinaipa kwambiri, chifukwa munachita zinthu zonyansa.+ Chotero dziko lanu linasanduka bwinja, chinthu chodabwitsa ndi chotembereredwa ndipo tsopano mulibe munthu wokhalamo.+

  • Ezekieli 6:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Ombani m’manja+ ndipo pondani pansi mwamphamvu ndi mapazi anu. Munene kuti: “Kalanga ine!” chifukwa cha zoipa zonse zonyansa za nyumba ya Isiraeli.+ Pakuti iwo adzaphedwa ndi lupanga,+ njala+ ndi mliri.+

  • Ezekieli 7:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Tsopano mapeto akufikira,+ ndipo ndikutumizira mkwiyo wanga. Ndikuweruza mogwirizana ndi njira zako+ ndipo ndikubwezera chifukwa cha zonyansa zako zonse.

  • Ezekieli 33:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Dzikolo ndikadzalisandutsa bwinja ndiponso malo owonongeka+ chifukwa cha zonyansa zonse zimene achita,+ iwo adzadziwa kuti ine ndine Yehova.”’

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena