Ezekieli 12:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Choncho uwauze kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Ine ndidzathetsa mwambi umenewu ndipo sadzaunenanso ngati mwambi mu Isiraeli.”’ Komano uwauze kuti, ‘Masiku ayandikira+ ndipo masomphenya onse adzakwaniritsidwa.’
23 Choncho uwauze kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Ine ndidzathetsa mwambi umenewu ndipo sadzaunenanso ngati mwambi mu Isiraeli.”’ Komano uwauze kuti, ‘Masiku ayandikira+ ndipo masomphenya onse adzakwaniritsidwa.’