Yoweli 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Lizani lipenga mu Ziyoni.+ Lengezani mʼphiri langa loyera kuti kukubwera nkhondo. Anthu onse okhala mʼdzikoli anjenjemere,Chifukwa tsiku la Yehova likubwera+ ndipo lili pafupi. Zefaniya 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsiku lalikulu la Yehova lili pafupi.+ Lili pafupi ndipo likubwera mofulumira kwambiri.+ Mkokomo wa tsiku la Yehova ukubwera ndi zowawa.+ Pa tsiku limenelo msilikali adzalira.+
2 “Lizani lipenga mu Ziyoni.+ Lengezani mʼphiri langa loyera kuti kukubwera nkhondo. Anthu onse okhala mʼdzikoli anjenjemere,Chifukwa tsiku la Yehova likubwera+ ndipo lili pafupi.
14 Tsiku lalikulu la Yehova lili pafupi.+ Lili pafupi ndipo likubwera mofulumira kwambiri.+ Mkokomo wa tsiku la Yehova ukubwera ndi zowawa.+ Pa tsiku limenelo msilikali adzalira.+