Ezekieli 13:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Uza anthu amene akupaka laimuwo kuti khomalo lidzagwa. Kudzagwa mvula yamphamvu, kudzagwanso matalala akuluakulu* ndipo mphepo yamkuntho idzagwetsa khomalo.+
11 Uza anthu amene akupaka laimuwo kuti khomalo lidzagwa. Kudzagwa mvula yamphamvu, kudzagwanso matalala akuluakulu* ndipo mphepo yamkuntho idzagwetsa khomalo.+