Ezekieli 14:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Iwe mwana wa munthu, amuna awa atsimikiza mumtima mwawo kuti azitsatira mafano awo onyansa,* ndipo aika chinthu chopunthwitsa chimene chimachititsa kuti anthu azichimwa. Kodi ndiwayankhe iwo akamandifunsa?+
3 “Iwe mwana wa munthu, amuna awa atsimikiza mumtima mwawo kuti azitsatira mafano awo onyansa,* ndipo aika chinthu chopunthwitsa chimene chimachititsa kuti anthu azichimwa. Kodi ndiwayankhe iwo akamandifunsa?+