Ezekieli 14:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Iwe mwana wa munthu, amuna awa aika mitima yawo pamafano onyansa, ndipo aika pamaso pawo chinthu chopunthwitsa chimene chimawalakwitsa.+ Kodi ndiwayankhe iwo akamandifunsa?+
3 “Iwe mwana wa munthu, amuna awa aika mitima yawo pamafano onyansa, ndipo aika pamaso pawo chinthu chopunthwitsa chimene chimawalakwitsa.+ Kodi ndiwayankhe iwo akamandifunsa?+