Ezekieli 7:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “‘Siliva wawo adzamuponyera mumsewu ndipo golide wawo adzaipidwa naye. Siliva wawo kapena golide wawo sadzatha kuwapulumutsa m’tsiku la mkwiyo waukulu wa Yehova.+ Iwo sadzakhuta ndipo m’matumbo mwawo simudzadzaza, pakuti chumacho chakhala chowapunthwitsa ndiponso chowachititsa zolakwa.+ Chivumbulutso 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “‘Koma ngakhale zili choncho, ndakupeza ndi milandu ingapo. Iwe kumeneko uli ndi anthu olimbikira chiphunzitso cha Balamu,+ amene anaphunzitsa Balaki+ kuikira ana a Isiraeli chopunthwitsa kuti adye zoperekedwa nsembe kwa mafano ndi kuchita dama.+
19 “‘Siliva wawo adzamuponyera mumsewu ndipo golide wawo adzaipidwa naye. Siliva wawo kapena golide wawo sadzatha kuwapulumutsa m’tsiku la mkwiyo waukulu wa Yehova.+ Iwo sadzakhuta ndipo m’matumbo mwawo simudzadzaza, pakuti chumacho chakhala chowapunthwitsa ndiponso chowachititsa zolakwa.+
14 “‘Koma ngakhale zili choncho, ndakupeza ndi milandu ingapo. Iwe kumeneko uli ndi anthu olimbikira chiphunzitso cha Balamu,+ amene anaphunzitsa Balaki+ kuikira ana a Isiraeli chopunthwitsa kuti adye zoperekedwa nsembe kwa mafano ndi kuchita dama.+