-
Ezekieli 44:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Ine ndatambasula dzanja langa kuti ndiwalange+ chifukwa chakuti anali kutumikira anthu pamaso pa mafano awo onyansa.+ Iwo anakhala chopunthwitsa kwa anthu a nyumba ya Isiraeli ndipo anawachititsa zinthu zoipa,+ choncho adzakumana ndi zotsatira za zochita zawo,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.
-