Yesaya 9:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Amene akutsogolera anthuwa ndiwo amene akuwasocheretsa,+ ndipo amene akutsogoleredwawo ndiwo amene akusokonezedwa.+ Malaki 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Koma inu mwapatuka panjira yoyenera.+ Mwalepheretsa anthu ambiri kutsatira chilamulo.+ Mwaphwanya pangano limene ndinapangana ndi Levi,”+ watero Yehova wa makamu.
16 Amene akutsogolera anthuwa ndiwo amene akuwasocheretsa,+ ndipo amene akutsogoleredwawo ndiwo amene akusokonezedwa.+
8 “Koma inu mwapatuka panjira yoyenera.+ Mwalepheretsa anthu ambiri kutsatira chilamulo.+ Mwaphwanya pangano limene ndinapangana ndi Levi,”+ watero Yehova wa makamu.