Yeremiya 18:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pakuti anthu anga andiiwala+ moti amapereka nsembe zautsi kwa chinthu chopanda pake,+ ndiponso amapunthwitsa anthu amene akuyenda panjira zawo,+ m’njira zakale,+ ndi kuwayendetsa m’njira zina, njira zokumbikakumbika. Luka 11:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 “Tsoka inu odziwa Chilamulo, chifukwa munalanda anthu kiyi yowathandiza kudziwa zinthu.+ Inuyo simunalowemo, ndipo ofuna kulowamo munawatsekereza!”+
15 Pakuti anthu anga andiiwala+ moti amapereka nsembe zautsi kwa chinthu chopanda pake,+ ndiponso amapunthwitsa anthu amene akuyenda panjira zawo,+ m’njira zakale,+ ndi kuwayendetsa m’njira zina, njira zokumbikakumbika.
52 “Tsoka inu odziwa Chilamulo, chifukwa munalanda anthu kiyi yowathandiza kudziwa zinthu.+ Inuyo simunalowemo, ndipo ofuna kulowamo munawatsekereza!”+