Ezekieli 14:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “‘Kapena nditati ndichititse zilombo zolusa zakutchire kudutsa mʼdzikolo nʼkupha anthu ambiri, nʼkulichititsa kuti likhale bwinja popanda munthu aliyense wodutsamo chifukwa cha zilombo zolusazo,+
15 “‘Kapena nditati ndichititse zilombo zolusa zakutchire kudutsa mʼdzikolo nʼkupha anthu ambiri, nʼkulichititsa kuti likhale bwinja popanda munthu aliyense wodutsamo chifukwa cha zilombo zolusazo,+