-
Ezekieli 14:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Komabe anthu ena amene adzatsale mʼdzikolo adzathawa nʼkupulumuka ndipo adzatulutsidwamo,+ kuphatikizapo ana aamuna ndi aakazi. Iwo akubwera kwa inu, ndipo mukadzaona njira zawo ndi zochita zawo mudzatonthozedwa ndithu pambuyo pa tsoka limene ndinabweretsa pa Yerusalemu ndiponso pambuyo pa zonse zimene ndinachitira mzindawo.
-