-
Ezekieli 15:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Kodi anthu amadula nthambi yake kuti ikhale mtengo wogwiritsa ntchito inayake? Kapena kodi angatenge kamtengo kake nʼkukakhomerera pakhoma kuti azikolowekapo ziwiya zosiyanasiyana?
-