-
Ezekieli 15:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Kodi anthu amadula nthambi yake kuti ikhale mtengo wogwiritsira ntchito inayake? Kapena kodi amatengapo kamtengo koti akhome pakhoma kuti azikolowekapo ziwiya zosiyanasiyana?
-