Ezekieli 19:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mkangowo unalera mwana wake wina ndipo mwanayo anakula nʼkukhala mkango wamphamvu.+ Anaphunzira kupha nyamaNdipo anayamba kudya ngakhale anthu.
3 Mkangowo unalera mwana wake wina ndipo mwanayo anakula nʼkukhala mkango wamphamvu.+ Anaphunzira kupha nyamaNdipo anayamba kudya ngakhale anthu.