Ezekieli 19:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “‘Patapita nthawi, mkangowo unalera mwana wake mmodzi mpaka kukula.+ Mwanayo anakhala mkango wamphamvu wamphongo. Anaphunzira kupha nyama+ ndipo anayamba kudya ngakhale anthu.
3 “‘Patapita nthawi, mkangowo unalera mwana wake mmodzi mpaka kukula.+ Mwanayo anakhala mkango wamphamvu wamphongo. Anaphunzira kupha nyama+ ndipo anayamba kudya ngakhale anthu.