Ezekieli 20:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Iwe mwana wa munthu, lankhula ndi akuluakulu a Isiraeliwo ndipo uwauze kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Kodi mwabwera kudzafunsira kwa ine? ‘Pali ine Mulungu wamoyo, sindikuyankhani,’+ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”’
3 “Iwe mwana wa munthu, lankhula ndi akuluakulu a Isiraeliwo ndipo uwauze kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Kodi mwabwera kudzafunsira kwa ine? ‘Pali ine Mulungu wamoyo, sindikuyankhani,’+ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”’