Yesaya 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Inu mukabwera kudzaonekera pamaso panga,+Kodi ndi ndani amene amakuuzani kuti muchite zimenezi,Ndi ndani amene amakuuzani kuti muzipondaponda mabwalo a panyumba panga?+ Yesaya 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndipo mukatambasula manja anu,Ndimakubisirani maso anga.+ Ngakhale mupereke mapemphero ambiri,+Ine sindimvetsera.+Manja anu adzaza magazi.+ Ezekieli 14:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Iwe mwana wa munthu, amuna awa atsimikiza mumtima mwawo kuti azitsatira mafano awo onyansa,* ndipo aika chinthu chopunthwitsa chimene chimachititsa kuti anthu azichimwa. Kodi ndiwayankhe iwo akamandifunsa?+
12 Inu mukabwera kudzaonekera pamaso panga,+Kodi ndi ndani amene amakuuzani kuti muchite zimenezi,Ndi ndani amene amakuuzani kuti muzipondaponda mabwalo a panyumba panga?+
15 Ndipo mukatambasula manja anu,Ndimakubisirani maso anga.+ Ngakhale mupereke mapemphero ambiri,+Ine sindimvetsera.+Manja anu adzaza magazi.+
3 “Iwe mwana wa munthu, amuna awa atsimikiza mumtima mwawo kuti azitsatira mafano awo onyansa,* ndipo aika chinthu chopunthwitsa chimene chimachititsa kuti anthu azichimwa. Kodi ndiwayankhe iwo akamandifunsa?+