Ezekieli 20:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kodi wakonzeka kuti uwaweruze? Kodi wakonzeka kuwaweruza, iwe mwana wa munthu? Auze zinthu zonyansa zimene makolo awo anachita.+
4 Kodi wakonzeka kuti uwaweruze? Kodi wakonzeka kuwaweruza, iwe mwana wa munthu? Auze zinthu zonyansa zimene makolo awo anachita.+