Ezekieli 20:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 chifukwa sanatsatire zigamulo zanga, anakana malamulo anga,+ anadetsa sabata langa ndiponso ankalambira mafano onyansa a makolo awo.+
24 chifukwa sanatsatire zigamulo zanga, anakana malamulo anga,+ anadetsa sabata langa ndiponso ankalambira mafano onyansa a makolo awo.+