Ezekieli 20:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndinawasiya kuti adziipitse ndi nsembe zawo pamene ankaponya pamoto mwana aliyense woyamba kubadwa.+ Ndinachita zimenezi kuti ndiwawononge nʼcholinga choti adziwe kuti ine ndine Yehova.”’
26 Ndinawasiya kuti adziipitse ndi nsembe zawo pamene ankaponya pamoto mwana aliyense woyamba kubadwa.+ Ndinachita zimenezi kuti ndiwawononge nʼcholinga choti adziwe kuti ine ndine Yehova.”’