Ezekieli 20:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndinawalola kudziipitsa ndi mphatso zawo pamene anali kuponya pamoto* mwana aliyense woyamba kubadwa.+ Ndinachita zimenezi kuti ndiwasautse n’cholinga choti adziwe kuti ine ndine Yehova.”’+
26 Ndinawalola kudziipitsa ndi mphatso zawo pamene anali kuponya pamoto* mwana aliyense woyamba kubadwa.+ Ndinachita zimenezi kuti ndiwasautse n’cholinga choti adziwe kuti ine ndine Yehova.”’+