-
Ezekieli 20:31Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
31 Ndipo mukupitiriza kudziipitsa mpaka lero popereka nsembe kwa mafano anu onse onyansa nʼkumawotcha ana anu pamoto.+ Ndiye kodi pa nthawi imodzimodziyo ndiyankhe zimene mukufunsa, inu a nyumba ya Isiraeli?”’+
‘Pali ine Mulungu wamoyo, sindiyankha zimene mukufunsazo,’+ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.
-