-
Ezekieli 20:31Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
31 Kodi mukudziipitsa polemekeza mafano anu onse onyansa mpaka lero,+ popereka mphatso zanu mwa kuponya pamoto ana anu aamuna?+ Kodi pa nthawi imodzimodziyo ndilole kuti mufunsire kwa ine, inu anthu a nyumba ya Isiraeli?”’+
“‘Pali ine Mulungu wamoyo, sindilola kuti mufunsire kwa ine,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.
-