1 Samueli 28:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ngakhale kuti anali kufunsira kwa Yehova,+ Yehova sanamuyankhe+ kaya kudzera m’maloto,+ Urimu+ kapena kudzera mwa aneneri.+ Miyambo 1:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Pa nthawi imeneyo azidzangondiitana koma sindidzayankha.+ Adzakhalira kundifunafuna koma sadzandipeza,+ Yesaya 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mukatambasula manja anu,+ ndimakubisirani maso anga.+ Ngakhale mupereke mapemphero ambiri,+ ine sindimvetsera.+ Manja anu adzaza magazi amene mwakhetsa.+
6 Ngakhale kuti anali kufunsira kwa Yehova,+ Yehova sanamuyankhe+ kaya kudzera m’maloto,+ Urimu+ kapena kudzera mwa aneneri.+
28 Pa nthawi imeneyo azidzangondiitana koma sindidzayankha.+ Adzakhalira kundifunafuna koma sadzandipeza,+
15 Mukatambasula manja anu,+ ndimakubisirani maso anga.+ Ngakhale mupereke mapemphero ambiri,+ ine sindimvetsera.+ Manja anu adzaza magazi amene mwakhetsa.+