-
Ezekieli 20:40Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
40 ‘Nyumba yonse ya Isiraeli idzanditumikira mʼphiri langa loyera,+ phiri lalitali lamʼdziko la Isiraeli,’+ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa. ‘Kumeneko ndidzasangalala nanu ndipo ndidzafuna kuti mundibweretsere zopereka zanu komanso nsembe zanu zabwino kwambiri za zinthu zanu zonse zopatulika.+
-