-
Ezekieli 23:44Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
44 Choncho amuna aja anapitiriza kupita kwa iye ngati mmene amuna amapitira kwa hule. Umu ndi mmene ankapitira kwa Ohola ndi Oholiba, akazi akhalidwe lonyansa.
-