Ezekieli 23:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Amuna aja anapitiriza kubwera kwa iye monga mmene amuna amapitira kwa hule. Anapita kwa Ohola ndi Oholiba monga akazi akhalidwe lotayirira.+
44 Amuna aja anapitiriza kubwera kwa iye monga mmene amuna amapitira kwa hule. Anapita kwa Ohola ndi Oholiba monga akazi akhalidwe lotayirira.+