Ezekieli 25:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Iwe mwana wa munthu, yangʼana kwa Aamoni+ ndipo ulosere zoipa zimene zidzawachitikire.+