Ezekieli 25:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: ‘Popeza Afilisiti akupitiriza kuchitira zoipa Aisiraeli chifukwa chodana nawo, iwo akufuna kubwezera komanso kuwononga Aisiraeliwo mwankhanza.*+
15 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: ‘Popeza Afilisiti akupitiriza kuchitira zoipa Aisiraeli chifukwa chodana nawo, iwo akufuna kubwezera komanso kuwononga Aisiraeliwo mwankhanza.*+