7 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Ine ndikutumiza Nebukadinezara mfumu ya Babulo, mfumu ya mafumu,+ kuchokera kumpoto+ kuti akaukire Turo. Iye adzapita ndi mahatchi,+ magaleta ankhondo,+ asilikali apamahatchi ndi gulu la asilikali ambiri.