Ezekieli 27:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Damasiko+ ankachita nawe malonda chifukwa choti unali ndi katundu komanso chuma chambiri. Ankakupatsa vinyo wa ku Heliboni komanso ubweya wa nkhosa wa ku Zahari posinthanitsa ndi katundu wako.
18 Damasiko+ ankachita nawe malonda chifukwa choti unali ndi katundu komanso chuma chambiri. Ankakupatsa vinyo wa ku Heliboni komanso ubweya wa nkhosa wa ku Zahari posinthanitsa ndi katundu wako.