Ezekieli 27:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “‘“Unali kuchita malonda ndi Damasiko+ pogulitsa katundu wambiri amene unali naye, pakuti unali ndi katundu wambiri wosiyanasiyana. Posinthana katundu, iye anakupatsa vinyo+ wa ku Heliboni ndi ubweya wa nkhosa wotuwa mofiirira.
18 “‘“Unali kuchita malonda ndi Damasiko+ pogulitsa katundu wambiri amene unali naye, pakuti unali ndi katundu wambiri wosiyanasiyana. Posinthana katundu, iye anakupatsa vinyo+ wa ku Heliboni ndi ubweya wa nkhosa wotuwa mofiirira.