Ezekieli 29:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Ndibweretsa lupanga mʼdziko lako+ ndipo ndidzapha anthu ndi nyama zomwe.
8 Choncho Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Ndibweretsa lupanga mʼdziko lako+ ndipo ndidzapha anthu ndi nyama zomwe.