-
Ezekieli 29:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 “Iwe mwana wa munthu, Nebukadinezara*+ mfumu ya Babulo anachititsa kuti asilikali ake agwire ntchito yaikulu pomenyana ndi Turo.+ Mutu wa msilikali aliyense unameteka ndipo mapewa awo ananyuka. Koma mfumuyo ndi asilikali akewo sanalandire malipiro aliwonse pa ntchito imene anagwira pomenyana ndi Turo.
-