Ezekieli 30:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndidzalimbitsa manja a mfumu* ya Babulo+ ndipo ndidzaipatsa lupanga langa.+ Ndidzathyola manja a Farao ndipo adzabuula kwambiri ngati munthu amene watsala pangʼono kufa pamaso pa mfumu ya Babulo.
24 Ndidzalimbitsa manja a mfumu* ya Babulo+ ndipo ndidzaipatsa lupanga langa.+ Ndidzathyola manja a Farao ndipo adzabuula kwambiri ngati munthu amene watsala pangʼono kufa pamaso pa mfumu ya Babulo.