-
Ezekieli 31:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Mbalame zonse zouluka mumlengalenga zinkamanga zisa zawo mʼnthambi zake,
Nyama zonse zakutchire zinkaberekera pansi pa nthambi zake,
Ndipo mitundu yonse ya anthu ambiri inkakhala mumthunzi wake.
-