Ezekieli 31:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Zolengedwa zonse zouluka m’mlengalenga zinali kumanga zisa zawo m’nthambi zake zikuluzikuluzo.+ Nyama zonse zakutchire zinkaberekera pansi pa nthambi zake.+ Mitundu yonse ya anthu ambiri inali kukhala mumthunzi wake.
6 Zolengedwa zonse zouluka m’mlengalenga zinali kumanga zisa zawo m’nthambi zake zikuluzikuluzo.+ Nyama zonse zakutchire zinkaberekera pansi pa nthambi zake.+ Mitundu yonse ya anthu ambiri inali kukhala mumthunzi wake.