Ezekieli 17:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndidzaibzala pamwamba pa phiri lalitali la ku Isiraeli+ ndipo idzachita nthambi ndi kubereka zipatso+ n’kukhala mtengo waukulu wa mkungudza.+ Mbalame zamitundu yonse zizidzakhala pansi pa mtengowo ndi mumthunzi wa masamba ake.+ Danieli 4:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Masamba ake anali okongola ndipo unali ndi zipatso zambiri. Mumtengomo munali zakudya zokwanira chamoyo chilichonse. Nyama zakutchire zinali kukhala pansi pake.+ Mbalame zam’mlengalenga zinali kukhala panthambi zake.
23 Ndidzaibzala pamwamba pa phiri lalitali la ku Isiraeli+ ndipo idzachita nthambi ndi kubereka zipatso+ n’kukhala mtengo waukulu wa mkungudza.+ Mbalame zamitundu yonse zizidzakhala pansi pa mtengowo ndi mumthunzi wa masamba ake.+
21 Masamba ake anali okongola ndipo unali ndi zipatso zambiri. Mumtengomo munali zakudya zokwanira chamoyo chilichonse. Nyama zakutchire zinali kukhala pansi pake.+ Mbalame zam’mlengalenga zinali kukhala panthambi zake.