-
Ezekieli 32:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 “Iwe mwana wa munthu, imba nyimbo yoimba polira yokhudza Farao, mfumu ya Iguputo ndipo umuuze kuti,
‘Iwe unali ngati mkango waungʼono wamphamvu* wa mitundu ina ya anthu,
Koma wakhalitsidwa chete.
Unali ngati chilombo chamʼnyanja+ chimene chimavundula madzi mwamphamvu mʼmitsinje yako
Nʼkumadetsa madzi ndi mapazi ako ndiponso kuipitsa mitsinjeyo.’
-