-
Ezekieli 32:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti:
‘Ndidzakuphimba ndi ukonde wanga pogwiritsa ntchito anthu a mitundu ina amene asonkhana pamodzi,
Ndipo iwo adzakukoka ndi khoka langa.
-