Ezekieli 32:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Ndidzakuphimba ndi ukonde+ wanga pogwiritsa ntchito khamu la anthu ambiri a mitundu ina, ndipo iwo adzakukola ndi khoka langa.+
3 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Ndidzakuphimba ndi ukonde+ wanga pogwiritsa ntchito khamu la anthu ambiri a mitundu ina, ndipo iwo adzakukola ndi khoka langa.+