12 Pakuti munthu+ nayenso sadziwa nthawi yake.+ Monga nsomba zimene zagwidwa mu ukonde wakupha,+ ndi mbalame zimene zakodwa mumsampha,+ ana a anthu nawonso amakodwa pa nthawi yatsoka,+ nthawiyo ikawafikira mwadzidzidzi.+
17 Kodi ndicho chifukwa chake adzapitirizabe kudzaza ndi kukhuthula nsomba za m’khoka lake? Kodi iye adzapitirizabe kupha mitundu ya anthu mopanda chifundo?+