2 Mbiri 36:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Choncho anawabweretsera mfumu ya Akasidi+ yomwe inapha anyamata awo ndi lupanga+ m’nyumba yopatulika.+ Sinachitire chisoni mnyamata kapena namwali, wachikulire kapena nkhalamba yotheratu.+ Mulungu anapereka zonse m’manja mwake. Nahumu 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Aliyense wokuona adzakuthawa+ ndipo adzanena kuti, ‘Nineve wasakazidwa! Ndani adzamuchitira chisoni?’ Kodi anthu oti akutonthoze ndiwapeza kuti?
17 Choncho anawabweretsera mfumu ya Akasidi+ yomwe inapha anyamata awo ndi lupanga+ m’nyumba yopatulika.+ Sinachitire chisoni mnyamata kapena namwali, wachikulire kapena nkhalamba yotheratu.+ Mulungu anapereka zonse m’manja mwake.
7 Aliyense wokuona adzakuthawa+ ndipo adzanena kuti, ‘Nineve wasakazidwa! Ndani adzamuchitira chisoni?’ Kodi anthu oti akutonthoze ndiwapeza kuti?