Ezekieli 32:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndidzawononga ziweto zake zonse zimene zili mʼmbali mwa madzi ambiri.+Ndipo phazi la munthu kapena ziboda za ziweto sizidzadetsanso madziwo.+
13 Ndidzawononga ziweto zake zonse zimene zili mʼmbali mwa madzi ambiri.+Ndipo phazi la munthu kapena ziboda za ziweto sizidzadetsanso madziwo.+