Ezekieli 29:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Ndibweretsa lupanga mʼdziko lako+ ndipo ndidzapha anthu ndi nyama zomwe. Ezekieli 29:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndipo munthu kapena chiweto sichidzadutsa mʼdziko lako,+ ndipo simudzakhala munthu aliyense kwa zaka 40.
8 Choncho Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Ndibweretsa lupanga mʼdziko lako+ ndipo ndidzapha anthu ndi nyama zomwe.
11 Ndipo munthu kapena chiweto sichidzadutsa mʼdziko lako,+ ndipo simudzakhala munthu aliyense kwa zaka 40.