Ezekieli 35:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pa nthawi imeneyo udzadziwa kuti ine Yehova, ndinamva mawu onse achipongwe amene unanenera mapiri a ku Isiraeli. Pamene unanena kuti, “Mapiri aja awonongedwa ndipo aperekedwa kwa ife kuti tiwadye.”*
12 Pa nthawi imeneyo udzadziwa kuti ine Yehova, ndinamva mawu onse achipongwe amene unanenera mapiri a ku Isiraeli. Pamene unanena kuti, “Mapiri aja awonongedwa ndipo aperekedwa kwa ife kuti tiwadye.”*