Ezekieli 35:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iwe udzadziwa kuti ine Yehova, ndinamva mawu onse achipongwe amene unanenera mapiri a ku Isiraeli.+ Pakuti iwe unanena kuti: “Mapiri aja awonongedwa. Aperekedwa kwa ife kuti akhale chakudya chathu.”+
12 Iwe udzadziwa kuti ine Yehova, ndinamva mawu onse achipongwe amene unanenera mapiri a ku Isiraeli.+ Pakuti iwe unanena kuti: “Mapiri aja awonongedwa. Aperekedwa kwa ife kuti akhale chakudya chathu.”+