Ezekieli 38:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Udzabweranso ndi Gomeri ndi magulu ake onse a asilikali, komanso ana a Togarima+ ochokera kumadera akutali kwambiri akumpoto. Iwo adzabwera ndi magulu awo onse a asilikali. Choncho iwe udzabwera ndi mitundu yambiri ya anthu.+
6 Udzabweranso ndi Gomeri ndi magulu ake onse a asilikali, komanso ana a Togarima+ ochokera kumadera akutali kwambiri akumpoto. Iwo adzabwera ndi magulu awo onse a asilikali. Choncho iwe udzabwera ndi mitundu yambiri ya anthu.+